Anthu ena amatengera zinthu pa m’gong’o – Chakwera
Mtsogoleri wa Malawi Congress Party Dr. Lazarus Chakwera wati wazindikira kuti pomwe adali m’boma padali anthu ena otengela zinthu pa m’gong’o. Iwo ati anthu otelowo amasokoneza zinthu. Malingana ndi a Chakwera, izi azizindikira pomwe atuluka m’boma. Iwo ati m’malo mokhala ndi team work, padali individualism. “Ngakhale pamudzi mfumu siyituma mwana m’modzi”, atelo a Chakwera. Malinga…
How sure are we
Only one outlet so far: treat it as unconfirmed. That doesn’t make it false; it may be new, or an exclusive.
Who reported it
No verification data yet
Checks run automatically as new sources are ingested.
Score bands
What moves the score
Not in the score: AI checks and reader flags. Verified is separate: two or more independent outlets and a score of at least 65%.
High · How we score this